Salimo 36:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mawu a pakamwa pake ndi opweteka ndi achinyengo.+Wasiya kugwiritsa ntchito nzeru zomuthandiza kuchita zinthu zabwino.+ Salimo 50:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwe umadana ndi malangizo,*+Ndipo umaponya mawu anga kunkhongo.+
3 Mawu a pakamwa pake ndi opweteka ndi achinyengo.+Wasiya kugwiritsa ntchito nzeru zomuthandiza kuchita zinthu zabwino.+