Ezekieli 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa tsiku limene unabadwa,+ chingwe chako cha pamchombo sichinadulidwe. Sanakusambitse kuti uyere, sanakupake mchere ndiponso sanakukulunge munsalu.
4 Pa tsiku limene unabadwa,+ chingwe chako cha pamchombo sichinadulidwe. Sanakusambitse kuti uyere, sanakupake mchere ndiponso sanakukulunge munsalu.