Oweruza 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno anthu a m’Gibeya anayamba kundiukira, ndipo usiku anazungulira nyumba imene ndinalimo. Iwo anali kufuna kupha ineyo, koma anagwirira mdzakazi wanga+ mpaka anafa.+ Hoseya 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aisiraeli azama nazo zinthu zowononga+ ngati m’masiku a Gibeya.+ Mulungu adzakumbukira zolakwa zawo+ ndipo adzawalanga chifukwa cha machimo awo.
5 Ndiyeno anthu a m’Gibeya anayamba kundiukira, ndipo usiku anazungulira nyumba imene ndinalimo. Iwo anali kufuna kupha ineyo, koma anagwirira mdzakazi wanga+ mpaka anafa.+
9 Aisiraeli azama nazo zinthu zowononga+ ngati m’masiku a Gibeya.+ Mulungu adzakumbukira zolakwa zawo+ ndipo adzawalanga chifukwa cha machimo awo.