Miyambo 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu wosasunthika pachilungamo adzapeza moyo,+ koma munthu wofunafuna zoipa adzafa.+ Yakobo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Komanso, chilungamo+ ndicho chipatso+ cha mbewu zimene anthu odzetsa mtendere+ amafesa mu mtendere.+
18 Komanso, chilungamo+ ndicho chipatso+ cha mbewu zimene anthu odzetsa mtendere+ amafesa mu mtendere.+