Miyambo 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu woipa amapeza malipiro achinyengo,+ koma wofesa chilungamo amapeza malipiro enieni.+