-
Genesis 28:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako Yakobo anagalamuka ku tulo take n’kunena kuti: “Ndithudi Yehova ali pamalo pano, koma ine sindinadziwe.”
-