2 Mafumu 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anapitiriza kudziikira zipilala zopatulika+ ndi mizati yopatulika+ paphiri lililonse lalitali,+ ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.+ Hoseya 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Efuraimu wachulukitsa maguwa ansembe ndipo wachimwa.+ Iye wakhala ndi maguwa ansembe ndipo wawonjezera machimo ake.+
10 Iwo anapitiriza kudziikira zipilala zopatulika+ ndi mizati yopatulika+ paphiri lililonse lalitali,+ ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.+
11 “Efuraimu wachulukitsa maguwa ansembe ndipo wachimwa.+ Iye wakhala ndi maguwa ansembe ndipo wawonjezera machimo ake.+