Yeremiya 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mitunduyo mukaiuze izi anthu inu: “Milungu+ imene sinapange kumwamba ndi dziko lapansi+ ndi imene idzawonongedwe padziko lapansi, pansi pa thambo.”
11 Mitunduyo mukaiuze izi anthu inu: “Milungu+ imene sinapange kumwamba ndi dziko lapansi+ ndi imene idzawonongedwe padziko lapansi, pansi pa thambo.”