Yesaya 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzangousiya kuti uwonongeke.+ Sindidzatengulira mitengo yake ndipo sindidzaulimanso.+ M’mundamo mudzamera tchire ndi zitsamba zaminga,+ ndipo ndidzalamula mitambo kuti isagwetsere mvula pamundawo.+
6 Ndidzangousiya kuti uwonongeke.+ Sindidzatengulira mitengo yake ndipo sindidzaulimanso.+ M’mundamo mudzamera tchire ndi zitsamba zaminga,+ ndipo ndidzalamula mitambo kuti isagwetsere mvula pamundawo.+