Yoweli 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Mitundu ya anthu inyamuke ndi kubwera kuchigwa cha Yehosafati,+ pakuti kumeneko ndidzakhala pansi kuti ndiweruze mitundu yonse ya anthu yokhala mozungulira.+
12 “Mitundu ya anthu inyamuke ndi kubwera kuchigwa cha Yehosafati,+ pakuti kumeneko ndidzakhala pansi kuti ndiweruze mitundu yonse ya anthu yokhala mozungulira.+