Salimo 69:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Anthu ofatsa adzaona zimenezi ndipo adzakondwera.+Inu amene mukutumikira Mulungu, mtima wanu ukhalenso ndi moyo.+ Miyambo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Bambo anga anali kundilangiza+ kuti: “Mtima wako+ ugwire mwamphamvu mawu anga.+ Sunga malamulo anga kuti upitirize kukhala ndi moyo.+ Yesaya 55:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tcherani khutu+ lanu ndipo bwerani kwa ine.+ Mvetserani ndipo mudzakhalabe ndi moyo.+ Ine ndidzachita nanu pangano lokhalapo mpaka kalekale+ lokhudza kukoma mtima kwanga kosatha kosonyezedwa kwa Davide, kumene kuli kokhulupirika.+
32 Anthu ofatsa adzaona zimenezi ndipo adzakondwera.+Inu amene mukutumikira Mulungu, mtima wanu ukhalenso ndi moyo.+
4 Bambo anga anali kundilangiza+ kuti: “Mtima wako+ ugwire mwamphamvu mawu anga.+ Sunga malamulo anga kuti upitirize kukhala ndi moyo.+
3 Tcherani khutu+ lanu ndipo bwerani kwa ine.+ Mvetserani ndipo mudzakhalabe ndi moyo.+ Ine ndidzachita nanu pangano lokhalapo mpaka kalekale+ lokhudza kukoma mtima kwanga kosatha kosonyezedwa kwa Davide, kumene kuli kokhulupirika.+