Yobu 36:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti iye amakoka madontho a madzi.+Madonthowo amasefeka n’kutsika ngati mvula ndi nkhungu, Mlaliki 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mitsinje*+ yonse imapita kunyanja+ koma nyanjayo sidzaza.+ Mitsinjeyo imabwerera kumalo kumene inachokera kuti ikayambirenso kuyenda.+
27 Pakuti iye amakoka madontho a madzi.+Madonthowo amasefeka n’kutsika ngati mvula ndi nkhungu, Mlaliki 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mitsinje*+ yonse imapita kunyanja+ koma nyanjayo sidzaza.+ Mitsinjeyo imabwerera kumalo kumene inachokera kuti ikayambirenso kuyenda.+
7 Mitsinje*+ yonse imapita kunyanja+ koma nyanjayo sidzaza.+ Mitsinjeyo imabwerera kumalo kumene inachokera kuti ikayambirenso kuyenda.+