Yoswa 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Potsirizira pake anauza a m’nyumba ya Zabidi kufika pamaso pa Mulungu, mwamuna aliyense wamphamvu payekhapayekha. Ndipo Akani mwana wa Karami, mwana wa Zabidi, mwana wa Zera, wa fuko la Yuda, anasankhidwa.+
18 Potsirizira pake anauza a m’nyumba ya Zabidi kufika pamaso pa Mulungu, mwamuna aliyense wamphamvu payekhapayekha. Ndipo Akani mwana wa Karami, mwana wa Zabidi, mwana wa Zera, wa fuko la Yuda, anasankhidwa.+