Genesis 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Motero Mulungu analenga zilombo zikuluzikulu za m’nyanja+ ndi chamoyo chilichonse chokhala mmenemo.+ Nyanja inatulutsa zimenezi zambirimbiri monga mwa mitundu yake.+ Analenganso chamoyo chilichonse chouluka monga mwa mtundu wake. Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino. Salimo 104:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 M’nyanja yakuya iyi ndiponso yotambalala,+Muli zinthu zoyenda zosawerengeka,+Muli zamoyo zazikulu ndi zazing’ono zomwe.+
21 Motero Mulungu analenga zilombo zikuluzikulu za m’nyanja+ ndi chamoyo chilichonse chokhala mmenemo.+ Nyanja inatulutsa zimenezi zambirimbiri monga mwa mitundu yake.+ Analenganso chamoyo chilichonse chouluka monga mwa mtundu wake. Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino.
25 M’nyanja yakuya iyi ndiponso yotambalala,+Muli zinthu zoyenda zosawerengeka,+Muli zamoyo zazikulu ndi zazing’ono zomwe.+