Ekisodo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+ Salimo 103:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi wachifundo ndi wachisomo,+Wosakwiya msanga ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+ Salimo 145:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi wachisomo ndi wachifundo,+Wosakwiya msanga ndi wosonyeza kukoma mtima kosatha komanso kwakukulu.+ Yoweli 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ng’ambani mitima yanu+ osati zovala zanu+ ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu pakuti iye ndi wachisomo, wachifundo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+ Ndithu, iye adzakumverani chisoni chifukwa cha tsokalo.+
6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+
8 Yehova ndi wachisomo ndi wachifundo,+Wosakwiya msanga ndi wosonyeza kukoma mtima kosatha komanso kwakukulu.+
13 Ng’ambani mitima yanu+ osati zovala zanu+ ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu pakuti iye ndi wachisomo, wachifundo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+ Ndithu, iye adzakumverani chisoni chifukwa cha tsokalo.+