Hoseya 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zowawa ngati za mkazi amene akubereka zidzamugwera.+ Iye ndi mwana wopanda nzeru+ chifukwa nthawi yoti abadwe ikakwana, sadzadziika pamalo amene ana amatulukira pochokera m’chiberekero.+
13 Zowawa ngati za mkazi amene akubereka zidzamugwera.+ Iye ndi mwana wopanda nzeru+ chifukwa nthawi yoti abadwe ikakwana, sadzadziika pamalo amene ana amatulukira pochokera m’chiberekero.+