Ezekieli 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Khoma limene amuna inu mwalipaka laimulo, ndidzaligwetsa lonse mpaka pansi moti maziko ake adzaonekera.+ Mzindawo udzawonongedwa ndithu, ndipo inuyo mudzathera pakati pake. Choncho mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+ Mateyu 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma iye anawayankha kuti: “Kodi simukuziona zinthu zonsezi? Ndithu ndikukuuzani, Pano sipadzatsala mwala uliwonse pamwamba pa mwala unzake umene sudzagwetsedwa.”+
14 Khoma limene amuna inu mwalipaka laimulo, ndidzaligwetsa lonse mpaka pansi moti maziko ake adzaonekera.+ Mzindawo udzawonongedwa ndithu, ndipo inuyo mudzathera pakati pake. Choncho mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+
2 Koma iye anawayankha kuti: “Kodi simukuziona zinthu zonsezi? Ndithu ndikukuuzani, Pano sipadzatsala mwala uliwonse pamwamba pa mwala unzake umene sudzagwetsedwa.”+