Yesaya 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa, wabweretsa tsiku lachisokonezo,+ la kugonjetsedwa+ ndiponso lothetsa nzeru+ m’chigwa cha masomphenya. Kumeneko mpanda ukugwetsedwa+ ndipo kufuula kukumvekera m’phiri.+ Luka 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Komanso, padzakhala zizindikiro padzuwa,+ mwezi ndi nyenyezi. Padziko lapansi anthu a mitundu ina adzazunzika, ndipo adzathedwa nzeru chifukwa cha mkokomo wa nyanja+ ndi kuwinduka kwake.+
5 Pakuti Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa, wabweretsa tsiku lachisokonezo,+ la kugonjetsedwa+ ndiponso lothetsa nzeru+ m’chigwa cha masomphenya. Kumeneko mpanda ukugwetsedwa+ ndipo kufuula kukumvekera m’phiri.+
25 “Komanso, padzakhala zizindikiro padzuwa,+ mwezi ndi nyenyezi. Padziko lapansi anthu a mitundu ina adzazunzika, ndipo adzathedwa nzeru chifukwa cha mkokomo wa nyanja+ ndi kuwinduka kwake.+