Ezekieli 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti munawomba m’manja+ ndi kuponda pansi mwamphamvu, komanso munasangalala ndi mtima wonyoza poona zimene zinachitikira dziko la Isiraeli,+ Chivumbulutso 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Okhala padziko lapansi adzakondwera+ kwambiri ndi imfa yawoyo. Iwo adzatumizirana+ mphatso, chifukwa aneneri awiriwa anazunza okhala padziko lapansi.
6 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti munawomba m’manja+ ndi kuponda pansi mwamphamvu, komanso munasangalala ndi mtima wonyoza poona zimene zinachitikira dziko la Isiraeli,+
10 Okhala padziko lapansi adzakondwera+ kwambiri ndi imfa yawoyo. Iwo adzatumizirana+ mphatso, chifukwa aneneri awiriwa anazunza okhala padziko lapansi.