Hoseya 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthuwo atenthetsa mitima yawo ngati kuti aibweretsa pafupi ndi ng’anjo yamoto.+ Mitima yawoyo ikutentha mkati mwawo.+ Wophika mkate akugona usiku wonse. Pofika m’mawa, ng’anjoyo ikuyaka moto walawilawi.+ Mateyu 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 M’mawa kutacha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu onse anakambirana ndi kugwirizana kuti aphe Yesu.+ Machitidwe 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kutacha, Ayuda anakonza chiwembu+ ndi kulumbira mwa kudzitemberera+ kuti sadya kapena kumwa kanthu kufikira atapha Paulo.+
6 Anthuwo atenthetsa mitima yawo ngati kuti aibweretsa pafupi ndi ng’anjo yamoto.+ Mitima yawoyo ikutentha mkati mwawo.+ Wophika mkate akugona usiku wonse. Pofika m’mawa, ng’anjoyo ikuyaka moto walawilawi.+
27 M’mawa kutacha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu onse anakambirana ndi kugwirizana kuti aphe Yesu.+
12 Kutacha, Ayuda anakonza chiwembu+ ndi kulumbira mwa kudzitemberera+ kuti sadya kapena kumwa kanthu kufikira atapha Paulo.+