Deuteronomo 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 chifukwa simunafike kumalo anu a mpumulo+ ndi kulandira cholowa chimene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.
9 chifukwa simunafike kumalo anu a mpumulo+ ndi kulandira cholowa chimene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.