Yeremiya 50:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iphani munthu wofesa mbewu mu Babulo,+ ndiponso amene akugwira chikwakwa nthawi yokolola. Aliyense adzabwerera kwa anthu a mtundu wake, ndipo aliyense adzathawira kudziko lakwawo chifukwa choopa lupanga loopsa.+ Zefaniya 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Iye adzatambasulira dzanja lake kumpoto ndipo adzawononga Asuri.+ Adzachititsa Nineve kukhala bwinja,+ kukhala dziko lopanda madzi ngati chipululu.
16 Iphani munthu wofesa mbewu mu Babulo,+ ndiponso amene akugwira chikwakwa nthawi yokolola. Aliyense adzabwerera kwa anthu a mtundu wake, ndipo aliyense adzathawira kudziko lakwawo chifukwa choopa lupanga loopsa.+
13 “Iye adzatambasulira dzanja lake kumpoto ndipo adzawononga Asuri.+ Adzachititsa Nineve kukhala bwinja,+ kukhala dziko lopanda madzi ngati chipululu.