Yesaya 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Msuri adzaphedwa ndi lupanga, koma osati la munthu. Lupanga lidzamudya, koma osati la munthu wochokera kufumbi.+ Iye adzathawa chifukwa cha lupangalo ndipo ana ake aamuna adzagwiritsidwa ntchito yaukapolo.
8 Msuri adzaphedwa ndi lupanga, koma osati la munthu. Lupanga lidzamudya, koma osati la munthu wochokera kufumbi.+ Iye adzathawa chifukwa cha lupangalo ndipo ana ake aamuna adzagwiritsidwa ntchito yaukapolo.