Yeremiya 46:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndilanga Amoni+ wa ku No,+ Farao, Iguputo pamodzi ndi milungu yake+ ndi mafumu ake.+ Ndilanga Farao ndi onse amene amamukhulupirira.’+ Ezekieli 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mzinda wa Patirosi+ ndidzausandutsa bwinja. Mzinda wa Zowani+ ndidzautentha ndi moto ndipo ndidzapereka ziweruzo mumzinda wa No.+
25 “Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndilanga Amoni+ wa ku No,+ Farao, Iguputo pamodzi ndi milungu yake+ ndi mafumu ake.+ Ndilanga Farao ndi onse amene amamukhulupirira.’+
14 Mzinda wa Patirosi+ ndidzausandutsa bwinja. Mzinda wa Zowani+ ndidzautentha ndi moto ndipo ndidzapereka ziweruzo mumzinda wa No.+