Salimo 137:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wodala ndi iye amene adzagwira ana ako ndi kuwaphwanya zidutswazidutswa+Mwa kuwawombetsa pathanthwe. Yesaya 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ana awo adzaphwanyidwaphwanyidwa, iwo akuona.+ Katundu wa m’nyumba zawo adzalandidwa, ndipo akazi awo adzagwiriridwa.+
9 Wodala ndi iye amene adzagwira ana ako ndi kuwaphwanya zidutswazidutswa+Mwa kuwawombetsa pathanthwe.
16 Ana awo adzaphwanyidwaphwanyidwa, iwo akuona.+ Katundu wa m’nyumba zawo adzalandidwa, ndipo akazi awo adzagwiriridwa.+