Yesaya 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinanyoza cholowa changa+ ndipo ndinawapereka m’manja mwako.+ Iwe sunawachitire chifundo.+ Munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+ Yeremiya 51:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndidzabwezera Babulo ndi anthu onse okhala m’dziko la Kasidi zoipa zonse zimene anachita ku Ziyoni anthu inu mukuona,”+ watero Yehova. Zekariya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndakwiyira kwambiri anthu a mitundu ina amene akukhala mwabata.+ Ndawakwiyira chifukwa chakuti ine ndinangokwiyira anthu anga pang’ono pokha,+ koma anthu amenewa anakulitsa tsoka la anthu angawo.”’+
6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinanyoza cholowa changa+ ndipo ndinawapereka m’manja mwako.+ Iwe sunawachitire chifundo.+ Munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+
24 Ndidzabwezera Babulo ndi anthu onse okhala m’dziko la Kasidi zoipa zonse zimene anachita ku Ziyoni anthu inu mukuona,”+ watero Yehova.
15 Ndakwiyira kwambiri anthu a mitundu ina amene akukhala mwabata.+ Ndawakwiyira chifukwa chakuti ine ndinangokwiyira anthu anga pang’ono pokha,+ koma anthu amenewa anakulitsa tsoka la anthu angawo.”’+