Yeremiya 25:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ngati angakakane kulandira chikhochi m’manja mwako kuti amwe ukawauze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Mumwabe basi.+
28 Ngati angakakane kulandira chikhochi m’manja mwako kuti amwe ukawauze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Mumwabe basi.+