Salimo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Kodi Mfumu yaulemerero imeneyi ndani?”+“Ndi Yehova, wanyonga ndi wamphamvu,+Yehova wamphamvu mu nkhondo.”+ Yesaya 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Fuula mwachisangalalo iwe mkazi wokhala mu Ziyoni, pakuti Woyera wa Isiraeli ndi wamkulu pakati pako.”+
8 “Kodi Mfumu yaulemerero imeneyi ndani?”+“Ndi Yehova, wanyonga ndi wamphamvu,+Yehova wamphamvu mu nkhondo.”+
6 “Fuula mwachisangalalo iwe mkazi wokhala mu Ziyoni, pakuti Woyera wa Isiraeli ndi wamkulu pakati pako.”+