Salimo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Adzachititsa ofatsa kutsatira zigamulo zake,+Ndipo adzaphunzitsa ofatsa kuyenda m’njira yake.+ Salimo 76:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene Mulungu ananyamuka ndi kupereka chiweruzo,+Kuti apulumutse anthu onse ofatsa padziko lapansi.+ [Seʹlah.] Mateyu 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Odala ndi anthu amene ali ofatsa,+ chifukwa adzalandira dziko lapansi.+
9 Pamene Mulungu ananyamuka ndi kupereka chiweruzo,+Kuti apulumutse anthu onse ofatsa padziko lapansi.+ [Seʹlah.]