-
2 Mafumu 23:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mfumuyo inachotsa ntchito ansembe a milungu yachilendo, amene mafumu a Yuda anawaika kuti azifukiza nsembe yautsi pamalo okwezeka m’mizinda ya Yuda ndi malo ozungulira Yerusalemu. Inachotsanso ntchito ansembe ofukiza nsembe yautsi kwa Baala,+ kwa dzuwa, kwa mwezi, kwa magulu a nyenyezi, ndi kwa khamu lonse la zinthu zakuthambo.+
-
-
Hoseya 10:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Anthu okhala ku Samariya adzachita mantha ndi fano la ku Beti-aveni+ la mwana wa ng’ombe. Pakuti anthuwo pamodzi ndi ansembe a mulungu wachilendo, amene anali kusangalala ndi fanolo chifukwa cha ulemerero wake, adzalilirira. Adzalirira fanolo chifukwa ulemerero wake udzachoka likadzatengedwa kupita kudziko lina.+
-