1 Mbiri 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ana amene Yekoniya anabereka ali mkaidi anali Salatiyeli,+ Luka 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 mwana wa Yoanani,mwana wa Resa,mwana wa Zerubabele,+mwana wa Salatiyeli,+mwana wa Neri,