Zekariya 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mngeloyo anandiyankha kuti: “Kodi sukudziwadi tanthauzo la zinthu zimenezi?” Pamenepo ine ndinati: “Inde sindikudziwa mbuyanga.”+
5 Mngeloyo anandiyankha kuti: “Kodi sukudziwadi tanthauzo la zinthu zimenezi?” Pamenepo ine ndinati: “Inde sindikudziwa mbuyanga.”+