Yesaya 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndidzachititsa kuti Aiguputo ayambane ndi Aiguputo anzawo. Aliyense adzamenyana ndi m’bale wake ndipo aliyense adzamenyana ndi mnzake. Mzinda udzamenyana ndi mzinda unzake ndipo ufumu udzamenyana ndi ufumu unzake.+ Amosi 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akatengedwa ndi adani awo kupita ku ukapolo, kumeneko ndidzalamula lupanga kuti liwaphe.+ Ndidzakhala tcheru kuti ndiwagwetsere tsoka osati kuwapatsa madalitso.+
2 “Ndidzachititsa kuti Aiguputo ayambane ndi Aiguputo anzawo. Aliyense adzamenyana ndi m’bale wake ndipo aliyense adzamenyana ndi mnzake. Mzinda udzamenyana ndi mzinda unzake ndipo ufumu udzamenyana ndi ufumu unzake.+
4 Akatengedwa ndi adani awo kupita ku ukapolo, kumeneko ndidzalamula lupanga kuti liwaphe.+ Ndidzakhala tcheru kuti ndiwagwetsere tsoka osati kuwapatsa madalitso.+