Genesis 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kudzera mwa mbewu yako,+ mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso* ndithu chifukwa chakuti wamvera mawu anga.’”+ Yesaya 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 M’tsiku limenelo, Isiraeli adzakhala gawo limodzi mwa magawo atatu, pamodzi ndi Iguputo ndi Asuri,+ kutanthauza kuti adzakhala dalitso padziko lapansi,+
18 Kudzera mwa mbewu yako,+ mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso* ndithu chifukwa chakuti wamvera mawu anga.’”+
24 M’tsiku limenelo, Isiraeli adzakhala gawo limodzi mwa magawo atatu, pamodzi ndi Iguputo ndi Asuri,+ kutanthauza kuti adzakhala dalitso padziko lapansi,+