Mateyu 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Senzani goli+ langa ndipo phunzirani kwa ine,+ chifukwa ndine wofatsa+ ndi wodzichepetsa, ndipo mudzatsitsimulidwa,+ Mateyu 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Uzani mwana wamkazi wa Ziyoni kuti, ‘Taona! Mfumu yako ikubwera kwa iwe.+ Ndi yofatsa+ ndipo yakwera bulu wamng’ono wamphongo, mwana wa nyama yonyamula katundu.’”+
29 Senzani goli+ langa ndipo phunzirani kwa ine,+ chifukwa ndine wofatsa+ ndi wodzichepetsa, ndipo mudzatsitsimulidwa,+
5 “Uzani mwana wamkazi wa Ziyoni kuti, ‘Taona! Mfumu yako ikubwera kwa iwe.+ Ndi yofatsa+ ndipo yakwera bulu wamng’ono wamphongo, mwana wa nyama yonyamula katundu.’”+