Yeremiya 31:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Chingwe choyezera+ chidzachokera kumeneko n’kulunjika kuphiri la Garebi ndipo chidzazungulira mpaka ku Gowa. Ezekieli 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako ananditengera kumeneko ndipo ndinaonako munthu wamwamuna. Munthuyo anali kuoneka wonyezimira ngati mkuwa.+ M’manja mwake munali chingwe cha fulakesi* ndi bango loyezera,+ ndipo anaima pachipata. Zekariya 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano ndinakweza maso ndipo ndinaona munthu ali ndi chingwe choyezera m’dzanja lake.+
39 Chingwe choyezera+ chidzachokera kumeneko n’kulunjika kuphiri la Garebi ndipo chidzazungulira mpaka ku Gowa.
3 Kenako ananditengera kumeneko ndipo ndinaonako munthu wamwamuna. Munthuyo anali kuoneka wonyezimira ngati mkuwa.+ M’manja mwake munali chingwe cha fulakesi* ndi bango loyezera,+ ndipo anaima pachipata.