Hoseya 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Efuraimu akupitiriza kunena kuti, ‘Inetu ndalemeradi,+ ndapeza zinthu zamtengo wapatali.+ Palibe amene angapeze cholakwa chachikulu pa ntchito zanga zonse.’+
8 Efuraimu akupitiriza kunena kuti, ‘Inetu ndalemeradi,+ ndapeza zinthu zamtengo wapatali.+ Palibe amene angapeze cholakwa chachikulu pa ntchito zanga zonse.’+