Zekariya 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Yehova Mulungu wanga wanena kuti, ‘Weta nkhosa zanga zimene zinayenera kuphedwa.+ Zekariya 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ndiyeno magawo awiri mwa magawo atatu a anthu a m’dziko lonseli adzaphedwa.+ Koma gawo lachitatu la anthuwo lidzatsalamo,”+ watero Yehova.
8 “Ndiyeno magawo awiri mwa magawo atatu a anthu a m’dziko lonseli adzaphedwa.+ Koma gawo lachitatu la anthuwo lidzatsalamo,”+ watero Yehova.