Ekisodo 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ngati yagunda kapolo wamwamuna kapena wamkazi, mwiniwake azilipira ndalama zokwana masekeli* 30+ kwa mbuye wa kapoloyo, ndipo ng’ombeyo iziponyedwa miyala. Maliko 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atamva zimenezo, iwo anasangalala ndi kumulonjeza kuti am’patsa ndalama zasiliva.+ Choncho iye anayamba kufunafuna mpata wabwino umene angamuperekere.+
32 Ngati yagunda kapolo wamwamuna kapena wamkazi, mwiniwake azilipira ndalama zokwana masekeli* 30+ kwa mbuye wa kapoloyo, ndipo ng’ombeyo iziponyedwa miyala.
11 Atamva zimenezo, iwo anasangalala ndi kumulonjeza kuti am’patsa ndalama zasiliva.+ Choncho iye anayamba kufunafuna mpata wabwino umene angamuperekere.+