Ezekieli 34:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndidzachita zimenezi chifukwa chakuti munali kukankha nkhosa ndi nthiti zanu ndiponso mapewa anu. Munali kugunda ndi nyanga zanu nkhosa zonse zodwala mpaka kuzibalalitsira kunja.+
21 Ndidzachita zimenezi chifukwa chakuti munali kukankha nkhosa ndi nthiti zanu ndiponso mapewa anu. Munali kugunda ndi nyanga zanu nkhosa zonse zodwala mpaka kuzibalalitsira kunja.+