-
Ezekieli 48:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 “Malire a mzindawo a mbali ya kum’mawa akhale mikono 4,500. Kumeneko kukhalenso zipata zitatu. Kukhale chipata chimodzi chotchedwa Yosefe, chipata chimodzi chotchedwa Benjamini, ndi chipata chimodzi chotchedwa Dani.
-