2 Mbiri 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ndidzasankha Yerusalemu+ kuti dzina langa likhale kumeneko, ndiponso ndidzasankha Davide kuti alamulire anthu anga Aisiraeli.’+ Zekariya 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova adzatenga Yuda kukhala gawo lake m’dziko loyera,+ ndipo adzasankha Yerusalemu.+
6 Koma ndidzasankha Yerusalemu+ kuti dzina langa likhale kumeneko, ndiponso ndidzasankha Davide kuti alamulire anthu anga Aisiraeli.’+