Yeremiya 31:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Pangano+ limene ndidzapangane ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa masiku amenewo ndi ili:+ Ndidzaika chilamulo changa mwa iwo+ ndipo ndidzachilemba mumtima mwawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga,”+ watero Yehova. Yohane 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho ndikupempha m’malo mwa iwo, sindikupemphera dziko,+ koma awo amene mwandipatsa, chifukwa iwo ndi anu.
33 “Pangano+ limene ndidzapangane ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa masiku amenewo ndi ili:+ Ndidzaika chilamulo changa mwa iwo+ ndipo ndidzachilemba mumtima mwawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga,”+ watero Yehova.
9 Choncho ndikupempha m’malo mwa iwo, sindikupemphera dziko,+ koma awo amene mwandipatsa, chifukwa iwo ndi anu.