Yeremiya 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “‘Koma ngakhale utasambira soda ndiponso sopo wambiri,+ cholakwa chako chidzaonekerabe ngati banga pamaso panga,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
22 “‘Koma ngakhale utasambira soda ndiponso sopo wambiri,+ cholakwa chako chidzaonekerabe ngati banga pamaso panga,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.