-
Mateyu 17:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Iye anati: “Inde amapereka.” Koma atalowa m’nyumba, asananene chilichonse, Yesu anamufunsa kuti: “Simoni, ukuganiza bwanji? Kodi mafumu a dziko lapansi amalandira ndalama za ziphaso kapena za msonkho kuchokera kwa ndani? Kuchokera kwa ana awo kapena kwa anthu achilendo?”
-