Luka 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno panali amuna 7 apachibale. Woyamba anatenga mkazi, koma anamwalira wopanda mwana.+