Maliko 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Koma pamene Yesu anali kuphunzitsa m’kachisi, anayankha zonse mwa kufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani alembi amanena kuti Khristu ndi mwana wa Davide?+
35 Koma pamene Yesu anali kuphunzitsa m’kachisi, anayankha zonse mwa kufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani alembi amanena kuti Khristu ndi mwana wa Davide?+