Luka 20:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndiyeno iye anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani amanena kuti Khristu ndi mwana wa Davide?+ Yohane 7:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kodi Malemba sanena kuti Khristu adzatuluka mwa ana a Davide,+ komanso mu Betelehemu+ mudzi umene Davide anali kukhala?”+
42 Kodi Malemba sanena kuti Khristu adzatuluka mwa ana a Davide,+ komanso mu Betelehemu+ mudzi umene Davide anali kukhala?”+