Mateyu 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Samalani kuti musamachite chilungamo chanu+ pamaso pa anthu ndi cholinga chakuti akuoneni, chifukwa mukatero simudzalandira mphoto kwa Atate wanu amene ali kumwamba.
6 “Samalani kuti musamachite chilungamo chanu+ pamaso pa anthu ndi cholinga chakuti akuoneni, chifukwa mukatero simudzalandira mphoto kwa Atate wanu amene ali kumwamba.