Numeri 15:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, uwauze kuti azisokerera mphonje m’mphepete mwa zovala zawo, ku mibadwo yawo yonse. Azisokereranso chingwe cha buluu pamwamba pa mphonje za zovalazo.+ Deuteronomo 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Uzimanga mphonje m’makona anayi a chovala chako.+
38 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, uwauze kuti azisokerera mphonje m’mphepete mwa zovala zawo, ku mibadwo yawo yonse. Azisokereranso chingwe cha buluu pamwamba pa mphonje za zovalazo.+